2 Mafumu 23:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma m’chaka cha 18 cha Mfumu Yosiya, iwo anachitira Yehova pasika ameneyu ku Yerusalemu.+