2 Mafumu 23:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Choncho atumiki ake ananyamula mtembo wake pagaleta kuchokera ku Megido n’kupita nawo ku Yerusalemu+ kumene anakauika m’manda ake. Kenako anthu a m’dzikolo anatenga Yehoahazi+ mwana wa Yosiya n’kumudzoza ndi kumulonga ufumu m’malo mwa bambo ake.
30 Choncho atumiki ake ananyamula mtembo wake pagaleta kuchokera ku Megido n’kupita nawo ku Yerusalemu+ kumene anakauika m’manda ake. Kenako anthu a m’dzikolo anatenga Yehoahazi+ mwana wa Yosiya n’kumudzoza ndi kumulonga ufumu m’malo mwa bambo ake.