Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 15:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Iye anali kuchita zoipa+ pamaso pa Yehova, ndipo anapitiriza kutsatira njira ya bambo ake+ ndi machimo awo amene anachimwitsa nawo Isiraeli.+

  • 1 Mafumu 22:52
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 52 Iye anapitiriza kuchita zoipa+ pamaso pa Yehova. Anayenda m’njira ya bambo ake,+ m’njira ya mayi ake,+ ndiponso m’njira ya Yerobowamu+ mwana wa Nebati, amene anachimwitsa Isiraeli.+

  • 2 Mafumu 15:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova.+ Sanasiye machimo a Yerobowamu+ mwana wa Nebati, amene anachimwitsa nawo Isiraeli.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena