Yeremiya 27:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma ngati iwo ndi aneneri, ndipo Yehova wawauza mawu, iwo achonderere kwa Yehova wa makamu+ kuti ziwiya zimene zinatsala m’nyumba ya Yehova, m’nyumba ya mfumu ya Yuda ndi zimene zinatsala ku Yerusalemu zisatengedwe kupita ku Babulo.’
18 Koma ngati iwo ndi aneneri, ndipo Yehova wawauza mawu, iwo achonderere kwa Yehova wa makamu+ kuti ziwiya zimene zinatsala m’nyumba ya Yehova, m’nyumba ya mfumu ya Yuda ndi zimene zinatsala ku Yerusalemu zisatengedwe kupita ku Babulo.’