1 Mafumu 8:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mwakwaniritsa lonjezo limene munalonjeza mtumiki wanu Davide bambo anga. Munalonjeza ndi pakamwa panu ndipo lero mwakwaniritsa ndi dzanja lanu.+
24 Mwakwaniritsa lonjezo limene munalonjeza mtumiki wanu Davide bambo anga. Munalonjeza ndi pakamwa panu ndipo lero mwakwaniritsa ndi dzanja lanu.+