Salimo 26:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti kukoma mtima kwanu kosatha kuli pamaso panga.Ine ndayenda m’choonadi chanu.+