1 Mafumu 8:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “Koma kodi Mulungu angakhaledi padziko lapansi?+ Taonani! Kumwamba,+ ngakhale kumwambamwamba,+ simungakwaneko.+ Kuli bwanji nyumba+ imene ndamangayi? Machitidwe 7:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Ngakhale ndi choncho, Wam’mwambamwamba sakhala m’nyumba zomangidwa ndi manja,+ monga mneneri akunenera kuti,
27 “Koma kodi Mulungu angakhaledi padziko lapansi?+ Taonani! Kumwamba,+ ngakhale kumwambamwamba,+ simungakwaneko.+ Kuli bwanji nyumba+ imene ndamangayi?
48 Ngakhale ndi choncho, Wam’mwambamwamba sakhala m’nyumba zomangidwa ndi manja,+ monga mneneri akunenera kuti,