Miyambo 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mtima umadziwa kuwawa kwa moyo wa munthu,+ ndipo mlendo sangalowerere pamene mtimawo ukusangalala.
10 Mtima umadziwa kuwawa kwa moyo wa munthu,+ ndipo mlendo sangalowerere pamene mtimawo ukusangalala.