1 Mafumu 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iweyo ukayenda+ pamaso panga monga momwe Davide+ bambo ako anayendera, yemwe anali ndi mtima wosagawanika+ ndipo anayenda mowongoka,+ ukachita mogwirizana ndi zonse zimene ndinakulamula,+ komanso ukasunga malangizo anga+ ndi zigamulo zanga,+ Salimo 26:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti kukoma mtima kwanu kosatha kuli pamaso panga.Ine ndayenda m’choonadi chanu.+
4 Iweyo ukayenda+ pamaso panga monga momwe Davide+ bambo ako anayendera, yemwe anali ndi mtima wosagawanika+ ndipo anayenda mowongoka,+ ukachita mogwirizana ndi zonse zimene ndinakulamula,+ komanso ukasunga malangizo anga+ ndi zigamulo zanga,+