2 Mbiri 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kuwonjezera apo, anakongoletsa nyumbayo+ poikuta ndi miyala yamtengo wapatali. Golide+ wakeyo anali wochokera kudziko la golide.
6 Kuwonjezera apo, anakongoletsa nyumbayo+ poikuta ndi miyala yamtengo wapatali. Golide+ wakeyo anali wochokera kudziko la golide.