1 Mafumu 4:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndipo anthu ankabwera kuchokera ku mitundu yonse kudzamva nzeru za Solomo,+ ngakhalenso kuchokera kwa mafumu onse a padziko lapansi amene anamva za nzeru zake.+
34 Ndipo anthu ankabwera kuchokera ku mitundu yonse kudzamva nzeru za Solomo,+ ngakhalenso kuchokera kwa mafumu onse a padziko lapansi amene anamva za nzeru zake.+