1 Mafumu 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mfumuyo inayamba kuyankha anthuwo mwaukali+ ndipo sinamvere malangizo ochokera kwa akulu amene anailangiza aja.+ Yobu 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kodi okalamba si paja amakhala ndi nzeru,+Ndipo amene akhala masiku ambiri si paja amamvetsa zinthu?
13 Mfumuyo inayamba kuyankha anthuwo mwaukali+ ndipo sinamvere malangizo ochokera kwa akulu amene anailangiza aja.+
12 Kodi okalamba si paja amakhala ndi nzeru,+Ndipo amene akhala masiku ambiri si paja amamvetsa zinthu?