Yesaya 22:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mudzawerenga nyumba za ku Yerusalemu ndipo mudzagwetsanso nyumba kuti mulimbitsire khoma lake.+