2 Mbiri 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yerobowamu+ mwana wa Nebati atamva zimenezi ali ku Iguputo,+ (pajatu anathawa mfumu Solomo,) nthawi yomweyo anabwerera kuchokera ku Iguputoko.+
2 Yerobowamu+ mwana wa Nebati atamva zimenezi ali ku Iguputo,+ (pajatu anathawa mfumu Solomo,) nthawi yomweyo anabwerera kuchokera ku Iguputoko.+