-
Yoswa 8:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Amuna a ku Ai atacheuka anangoona utsi uli tolo mumzindawo, ndipo anasoweratu mphamvu zoti n’kuthawira kwina kulikonse. Pamenepo asilikali achiisiraeli amene ankathawira kuchipululu aja, anatembenukira amuna a ku Aiwo.
-