Mlaliki 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kuli bwino kuti usalonjeze+ kusiyana ndi kulonjeza koma osakwaniritsa zimene walonjezazo.+ Mateyu 5:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 “Komanso munamva kuti anthu akale anauzidwa kuti, ‘Usamalumbire+ koma osachita, m’malomwake uzikwaniritsa malonjezo ako kwa Yehova.’+
33 “Komanso munamva kuti anthu akale anauzidwa kuti, ‘Usamalumbire+ koma osachita, m’malomwake uzikwaniritsa malonjezo ako kwa Yehova.’+