Ekisodo 31:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndidzam’patsa mzimuwo kutinso akhale wotha kulinganiza kapangidwe ka zinthu, kupanga zinthu zagolide, zasiliva ndi zamkuwa,+ Ekisodo 35:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Anam’patsa mzimuwo kutinso akhale wotha kulinganiza kapangidwe ka zinthu, kupanga zinthu zagolide, zasiliva ndi zamkuwa,+
4 Ndidzam’patsa mzimuwo kutinso akhale wotha kulinganiza kapangidwe ka zinthu, kupanga zinthu zagolide, zasiliva ndi zamkuwa,+
32 Anam’patsa mzimuwo kutinso akhale wotha kulinganiza kapangidwe ka zinthu, kupanga zinthu zagolide, zasiliva ndi zamkuwa,+