2 Mbiri 11:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 M’mizinda yonse yosiyanasiyana anaikamo zishango zazikulu+ ndi mikondo ing’onoing’ono.+ Mizindayo anailimbitsa kwambiri, ndipo iye anapitiriza kulamulira Yuda ndi Benjamini. 2 Mbiri 11:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Komabe anachita mozindikira+ chifukwa anagawa ana akewo n’kuwaika m’madera onse a ku Yuda ndi ku Benjamini.+ Anawaika m’mizinda yonse yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri,+ ndipo anawapatsa chakudya chambiri+ ndi kuwapezera akazi ambirimbiri.+
12 M’mizinda yonse yosiyanasiyana anaikamo zishango zazikulu+ ndi mikondo ing’onoing’ono.+ Mizindayo anailimbitsa kwambiri, ndipo iye anapitiriza kulamulira Yuda ndi Benjamini.
23 Komabe anachita mozindikira+ chifukwa anagawa ana akewo n’kuwaika m’madera onse a ku Yuda ndi ku Benjamini.+ Anawaika m’mizinda yonse yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri,+ ndipo anawapatsa chakudya chambiri+ ndi kuwapezera akazi ambirimbiri.+