1 Mbiri 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Tsopano anagawa ana a Aroni m’magulu awo. Ana a Aroni anali Nadabu,+ Abihu,+ Eleazara,+ ndi Itamara.+
24 Tsopano anagawa ana a Aroni m’magulu awo. Ana a Aroni anali Nadabu,+ Abihu,+ Eleazara,+ ndi Itamara.+