Nehemiya 7:66 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 66 Mpingo wonsewo monga gulu limodzi unali ndi anthu 42,360,+ Yeremiya 23:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Ine ndidzasonkhanitsa pamodzi nkhosa zanga zotsala kuchokera m’mayiko onse kumene ndinazibalalitsira+ ndipo ndidzazibwezeretsa kumalo awo kumene zimadyera.+ Nkhosazo zidzaberekana ndi kuchuluka.+
3 “Ine ndidzasonkhanitsa pamodzi nkhosa zanga zotsala kuchokera m’mayiko onse kumene ndinazibalalitsira+ ndipo ndidzazibwezeretsa kumalo awo kumene zimadyera.+ Nkhosazo zidzaberekana ndi kuchuluka.+