Zekariya 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Manja a Zerubabele anayala maziko a nyumbayi,+ ndipo manja ake omwewo adzaimalizitsa.+ Pamenepo mudzadziwa kuti Yehova wa makamu wandituma kwa inu.+
9 “Manja a Zerubabele anayala maziko a nyumbayi,+ ndipo manja ake omwewo adzaimalizitsa.+ Pamenepo mudzadziwa kuti Yehova wa makamu wandituma kwa inu.+