Salimo 126:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Amene akupita kumunda akulira,+Atasenza thumba lodzaza mbewu,+Adzabwerako akufuula mosangalala,+Atasenza mtolo wake wa zokolola.+
6 Amene akupita kumunda akulira,+Atasenza thumba lodzaza mbewu,+Adzabwerako akufuula mosangalala,+Atasenza mtolo wake wa zokolola.+