Genesis 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ufumu wake unayambira ku Babele,+ Ereke,+ Akadi mpaka ku Kaline m’dziko la Sinara.+