Danieli 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mfumuyo inayankha Akasidiwo kuti: “Ine ndikulamula kuti: Amuna inu mukapanda kundiuza malotowo ndi kuwamasulira, mudzadulidwa nthulinthuli+ ndipo nyumba zanu zidzasanduka zimbudzi za anthu onse.+
5 Mfumuyo inayankha Akasidiwo kuti: “Ine ndikulamula kuti: Amuna inu mukapanda kundiuza malotowo ndi kuwamasulira, mudzadulidwa nthulinthuli+ ndipo nyumba zanu zidzasanduka zimbudzi za anthu onse.+