Zekariya 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pa tsiku la 24, m’mwezi wa 11 womwe ndi mwezi wa Sebati, m’chaka chachiwiri cha ulamuliro wa Dariyo,+ Yehova anaonetsa masomphenya mneneri Zekariya,+ mwana wa Berekiya, mwana wa Ido.+ Masomphenya amene ndinaonawo ndi awa:
7 Pa tsiku la 24, m’mwezi wa 11 womwe ndi mwezi wa Sebati, m’chaka chachiwiri cha ulamuliro wa Dariyo,+ Yehova anaonetsa masomphenya mneneri Zekariya,+ mwana wa Berekiya, mwana wa Ido.+ Masomphenya amene ndinaonawo ndi awa: