Ezara 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mulungu amene anaika dzina lake+ kumeneko, achotse mfumu iliyonse ndi anthu alionse ophwanya lamulo limeneli ndiponso owononga+ nyumba ya Mulungu imene ili ku Yerusalemu. Ine Dariyo ndaika lamulo limeneli, ndipo zichitike mwamsanga.”
12 Mulungu amene anaika dzina lake+ kumeneko, achotse mfumu iliyonse ndi anthu alionse ophwanya lamulo limeneli ndiponso owononga+ nyumba ya Mulungu imene ili ku Yerusalemu. Ine Dariyo ndaika lamulo limeneli, ndipo zichitike mwamsanga.”