Ezara 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Panalinso Zekariya kuchokera pa ana a Sekaniya, yemwe anali wochokera pa ana a Parosi.+ Iye anali ndi amuna amene analembetsa mayina awo okwanira 150. Nehemiya 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ana a Parosi,+ 2,172. Nehemiya 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Atsogoleri awa a anthu anatsimikiziranso panganoli: Parosi, Pahati-mowabu,+ Elamu, Zatu, Bani,
3 Panalinso Zekariya kuchokera pa ana a Sekaniya, yemwe anali wochokera pa ana a Parosi.+ Iye anali ndi amuna amene analembetsa mayina awo okwanira 150.