1 Mbiri 6:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Anthuwa anali ndi udindo+ woyang’anira oimba+ pachihema chopatulika kapena kuti chihema chokumanako, mpaka pamene Solomo anamanga nyumba ya Yehova ku Yerusalemu.+ Iwo anapitiriza kutumikira malinga ndi ntchito yawo.+
32 Anthuwa anali ndi udindo+ woyang’anira oimba+ pachihema chopatulika kapena kuti chihema chokumanako, mpaka pamene Solomo anamanga nyumba ya Yehova ku Yerusalemu.+ Iwo anapitiriza kutumikira malinga ndi ntchito yawo.+