Ezara 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pa ana a Bebai+ panali Zekariya mwana wa Bebai. Iye anali ndi amuna 28. Nehemiya 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ana a Bebai,+ 628.