Ezara 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pa ana a Azigadi+ panali Yohanani mwana wa Hakatani. Iye anali ndi amuna 110. Nehemiya 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ana a Azigadi,+ 2,322.