Ezara 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 ndi kutinso munyamule siliva ndi golide zimene mfumu ndi aphungu ake apereka mwaufulu+ kwa Mulungu wa Isiraeli, amene amakhala ku Yerusalemu.+
15 ndi kutinso munyamule siliva ndi golide zimene mfumu ndi aphungu ake apereka mwaufulu+ kwa Mulungu wa Isiraeli, amene amakhala ku Yerusalemu.+