Ezara 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Munyamulenso siliva ndi golide yense amene mum’peze m’chigawo chonse cha Babulo, limodzi ndi mphatso za anthu+ ndi za ansembe omwe akupereka mwaufulu kunyumba ya Mulungu wawo,+ yomwe ili ku Yerusalemu.
16 Munyamulenso siliva ndi golide yense amene mum’peze m’chigawo chonse cha Babulo, limodzi ndi mphatso za anthu+ ndi za ansembe omwe akupereka mwaufulu kunyumba ya Mulungu wawo,+ yomwe ili ku Yerusalemu.