Ezara 7:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Ineyo mfumu Aritasasita ndalamula+ asungichuma onse+ amene ali kutsidya lina la Mtsinje,*+ kuti chilichonse chimene wansembe Ezara,+ wokopera chilamulo cha Mulungu wakumwamba, angapemphe kwa inu chichitidwe mwamsanga.
21 “Ineyo mfumu Aritasasita ndalamula+ asungichuma onse+ amene ali kutsidya lina la Mtsinje,*+ kuti chilichonse chimene wansembe Ezara,+ wokopera chilamulo cha Mulungu wakumwamba, angapemphe kwa inu chichitidwe mwamsanga.