Ekisodo 34:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako mudzatenga ena mwa ana awo aakazi kuti akhale akazi a ana anu aamuna,+ ndipo ana awo aakazi adzachita chiwerewere ndi milungu yawo, n’kuchititsa ana anu aamuna kuchita chiwerewere ndi milungu yawo.+ Ezara 10:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Onsewa anali atatenga akazi achilendo,+ ndipo akaziwo ndi ana awo anawatumiza kwawo.
16 Kenako mudzatenga ena mwa ana awo aakazi kuti akhale akazi a ana anu aamuna,+ ndipo ana awo aakazi adzachita chiwerewere ndi milungu yawo, n’kuchititsa ana anu aamuna kuchita chiwerewere ndi milungu yawo.+