Salimo 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyang’aneni. Ndiyankheni, inu Yehova Mulungu wanga.Walitsani maso anga+ kuti ndisagone mu imfa.+