1 Mbiri 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pa ansembe panali Yedaya, Yehoyaribu, Yakini,+ 1 Mbiri 24:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Atachita maere, zotsatira zake zinali motere: Woyamba anali Yehoyaribu,+ wachiwiri Yedaya, Nehemiya 11:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakati pa ansembe panali awa: Yedaya mwana wa Yoyaribi,+ Yakini,+