Nehemiya 9:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Zokolola za m’dzikoli zachulukira+ mafumu+ amene mwatiikira chifukwa cha machimo athu.+ Iwo akulamulira matupi athu komanso ziweto zathu mmene akufunira, ndipo tili pamavuto aakulu.+
37 Zokolola za m’dzikoli zachulukira+ mafumu+ amene mwatiikira chifukwa cha machimo athu.+ Iwo akulamulira matupi athu komanso ziweto zathu mmene akufunira, ndipo tili pamavuto aakulu.+