Ekisodo 34:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako mudzatenga ena mwa ana awo aakazi kuti akhale akazi a ana anu aamuna,+ ndipo ana awo aakazi adzachita chiwerewere ndi milungu yawo, n’kuchititsa ana anu aamuna kuchita chiwerewere ndi milungu yawo.+ Deuteronomo 23:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Muamoni kapena Mmowabu asalowe mumpingo wa Yehova.+ Ana awo asalowe mumpingo wa Yehova kufikira m’badwo wa 10, ngakhalenso mpaka kalekale.
16 Kenako mudzatenga ena mwa ana awo aakazi kuti akhale akazi a ana anu aamuna,+ ndipo ana awo aakazi adzachita chiwerewere ndi milungu yawo, n’kuchititsa ana anu aamuna kuchita chiwerewere ndi milungu yawo.+
3 “Muamoni kapena Mmowabu asalowe mumpingo wa Yehova.+ Ana awo asalowe mumpingo wa Yehova kufikira m’badwo wa 10, ngakhalenso mpaka kalekale.