Yoswa 15:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Keila,+ Akizibu,+ ndi Maresha.+ Mizinda 9 ndi midzi yake. 1 Samueli 23:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Patapita nthawi, kunabwera anthu amene anauza Davide kuti: “Afilisiti akuthira nkhondo mzinda wa Keila,+ ndipo akufunkha zokolola zimene zili pamalo opunthira mbewu.”+ 1 Mbiri 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ana a mkazi wa Hodiya, mlongo wake wa Nahamu, anali bambo wa Keila+ Mgarimi, ndi Esitemowa Mmaakati.
23 Patapita nthawi, kunabwera anthu amene anauza Davide kuti: “Afilisiti akuthira nkhondo mzinda wa Keila,+ ndipo akufunkha zokolola zimene zili pamalo opunthira mbewu.”+
19 Ana a mkazi wa Hodiya, mlongo wake wa Nahamu, anali bambo wa Keila+ Mgarimi, ndi Esitemowa Mmaakati.