9 Kuwonjezera apo Uziya anamanga nsanja+ ku Yerusalemu pafupi ndi Chipata cha Pakona,+ Chipata cha Kuchigwa,+ ndiponso pafupi ndi Mchirikizo wa Khoma, ndipo nsanjazo anazilimbitsa.
24 Kenako, Binui mwana wamwamuna wa Henadadi anakonza gawo lina la mpandawo kuchokera panyumba ya Azariya kukafika ku Mchirikizo wa Khoma+ ndi kukona ya mpanda wa mzindawo.