Salimo 129:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Onse odana ndi Ziyoni,+Adzachita manyazi ndipo adzatembenuka ndi kubwerera okha.+