Nehemiya 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno Haneni+ mmodzi mwa abale anga anabwera pamodzi ndi amuna ena kuchokera ku Yuda. Ndinawafunsa+ mmene zinthu zinalili kwa gulu la Ayuda+ amene anathawa+ ku ukapolo+ komanso ndinawafunsa za Yerusalemu.
2 Ndiyeno Haneni+ mmodzi mwa abale anga anabwera pamodzi ndi amuna ena kuchokera ku Yuda. Ndinawafunsa+ mmene zinthu zinalili kwa gulu la Ayuda+ amene anathawa+ ku ukapolo+ komanso ndinawafunsa za Yerusalemu.