Yoswa 21:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Anatoti+ ndi malo ake odyetserako ziweto, ndiponso Alimoni+ ndi malo ake odyetserako ziweto. Yonse pamodzi inalipo mizinda inayi. Ezara 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Amuna a ku Anatoti,+ 128. Yeremiya 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Mawu a Yeremiya+ mwana wa Hilikiya,* mmodzi wa ansembe a ku Anatoti,+ m’dera la Benjamini.+
18 Anatoti+ ndi malo ake odyetserako ziweto, ndiponso Alimoni+ ndi malo ake odyetserako ziweto. Yonse pamodzi inalipo mizinda inayi.