Ezara 2:62 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 62 Amenewa ndiwo anayang’ana mayina awo m’kaundula kuti atsimikizire anthu onse za mzere wawo wobadwira koma sanapezekemo. Zitatero anawaletsa kuti asatumikire monga ansembe chifukwa anali oipitsidwa.+
62 Amenewa ndiwo anayang’ana mayina awo m’kaundula kuti atsimikizire anthu onse za mzere wawo wobadwira koma sanapezekemo. Zitatero anawaletsa kuti asatumikire monga ansembe chifukwa anali oipitsidwa.+