2 Mbiri 35:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pambuyo pake anakonza nyama yawo ndi ya ansembe+ chifukwa ansembe, ana a Aroni, anali otanganidwa ndi kupereka nsembe zopsereza+ ndiponso mafuta+ mpaka usiku. Choncho Alevi anakonza+ nyama yawo ndi ya ansembe, ana a Aroni.
14 Pambuyo pake anakonza nyama yawo ndi ya ansembe+ chifukwa ansembe, ana a Aroni, anali otanganidwa ndi kupereka nsembe zopsereza+ ndiponso mafuta+ mpaka usiku. Choncho Alevi anakonza+ nyama yawo ndi ya ansembe, ana a Aroni.