-
Luka 4:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Pamenepo anamupatsa mpukutu wa mneneri Yesaya. Iye anafunyulula mpukutuwo ndi kupeza pamene panalembedwa mawu akuti:
-