Nehemiya 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iwo anapitiriza kuwerenga+ bukulo mokweza. Anapitiriza kuwerenga chilamulo cha Mulungu woona, kuchifotokozera ndi kumveketsa tanthauzo lake. Iwo anapitiriza kuthandiza anthuwo kumvetsa tanthauzo la zimene anali kuwerenga.+
8 Iwo anapitiriza kuwerenga+ bukulo mokweza. Anapitiriza kuwerenga chilamulo cha Mulungu woona, kuchifotokozera ndi kumveketsa tanthauzo lake. Iwo anapitiriza kuthandiza anthuwo kumvetsa tanthauzo la zimene anali kuwerenga.+