Genesis 40:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho anafunsa atumiki a Farao aja, omwe anali naye m’ndende ya kunyumba kwa mbuye wakeyo, kuti: “N’chifukwa chiyani nkhope zanu zili zachisoni lero?”+
7 Choncho anafunsa atumiki a Farao aja, omwe anali naye m’ndende ya kunyumba kwa mbuye wakeyo, kuti: “N’chifukwa chiyani nkhope zanu zili zachisoni lero?”+