Salimo 72:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Lidalitsike dzina lake laulemerero mpaka kalekale,+Ndipo ulemerero wake udzaze dziko lonse lapansi.+Ame! Ame!* Salimo 145:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 145 Ndidzakukwezani, inu Mfumu ndi Mulungu wanga,+Ndipo ndidzatamanda dzina lanu mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+
19 Lidalitsike dzina lake laulemerero mpaka kalekale,+Ndipo ulemerero wake udzaze dziko lonse lapansi.+Ame! Ame!*
145 Ndidzakukwezani, inu Mfumu ndi Mulungu wanga,+Ndipo ndidzatamanda dzina lanu mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+