Genesis 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iyi ndi nkhani yofotokoza mmene kumwamba ndi dziko lapansi zinalengedwera, m’tsiku limene Yehova Mulungu anapanga dziko lapansi ndi kumwamba.+
4 Iyi ndi nkhani yofotokoza mmene kumwamba ndi dziko lapansi zinalengedwera, m’tsiku limene Yehova Mulungu anapanga dziko lapansi ndi kumwamba.+